Catholic Shona Hymn 20

Ambuye Ndabwera- Fr R.T Mabiri

M Nazo zinyai zokha Zochitikha paMisa (x2)

Cantor:

All Ambuye ndabwera Ambuye ndabwera Kudzapeleka Mpatso zanga, kwainu Ambuye x2

1. Choyambira ndiichi, Kupembedza Mulungu x2
2. Chachiwiri ndiichi, Kupepesa Mulungu x2
3. Chachitatu ndiichi, Kupemphera Mulungu x2
4. Chachinayi ndiichi, Kutokhoza Mulungu x2

Hymn Details

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

This site uses Akismet to reduce spam. Learn how your comment data is processed.